Deuteronomo 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova adzakuchotserani matenda onse. Ndipo sadzakugwetserani matenda onse oipa a ku Iguputo amene inu mukuwadziwa,+ koma adzawagwetsera pa onse odana nanu. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:15 Nsanja ya Olonda,6/15/1991, tsa. 4
15 Yehova adzakuchotserani matenda onse. Ndipo sadzakugwetserani matenda onse oipa a ku Iguputo amene inu mukuwadziwa,+ koma adzawagwetsera pa onse odana nanu.