Deuteronomo 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Muonetsetse kuti mukusunga lamulo lililonse limene ndikukupatsani lero,+ kuti mupitirize kukhala ndi moyo+ ndi kuti muchulukanedi, n’kupita kukatenga dziko limene Yehova analumbirira makolo anu.+
8 “Muonetsetse kuti mukusunga lamulo lililonse limene ndikukupatsani lero,+ kuti mupitirize kukhala ndi moyo+ ndi kuti muchulukanedi, n’kupita kukatenga dziko limene Yehova analumbirira makolo anu.+