-
Deuteronomo 12:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Koma udzazidyera pamaso pa Yehova Mulungu wako, pamalo amene Yehova Mulungu wako adzasankhe.+ Udzazidyera pamalowo iweyo, mwana wako wamwamuna, mwana wako wamkazi, kapolo wako wamwamuna, kapolo wako wamkazi ndi Mlevi wokhala mumzinda wanu. Ndipo uzidzasangalala+ pamaso pa Yehova Mulungu wako pa zochita zako zonse.
-