Deuteronomo 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 ‘Pakati panu papezeka anthu opanda pake+ amene akufuna kupatutsa anthu mumzinda wawo,+ ponena kuti: “Tiyeni tikatumikire milungu ina,” milungu imene inu simunaidziwe,’
13 ‘Pakati panu papezeka anthu opanda pake+ amene akufuna kupatutsa anthu mumzinda wawo,+ ponena kuti: “Tiyeni tikatumikire milungu ina,” milungu imene inu simunaidziwe,’