Deuteronomo 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Usapereke kwa Yehova Mulungu wako nsembe ya ng’ombe kapena nkhosa yokhala ndi chilema kapena vuto lililonse, chifukwa zimenezi ndi zonyansa kwa Yehova Mulungu wako.+
17 “Usapereke kwa Yehova Mulungu wako nsembe ya ng’ombe kapena nkhosa yokhala ndi chilema kapena vuto lililonse, chifukwa zimenezi ndi zonyansa kwa Yehova Mulungu wako.+