Deuteronomo 17:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Azichita zimenezi kuti mtima wake usadzikweze pamaso pa abale ake,+ komanso kuti asachoke pachilamulo mwa kupatukira kudzanja lamanja kapena lamanzere.+ Azichita zimenezi kuti iyeyo ndi ana ake atalikitse masiku a ufumu wawo+ mu Isiraeli. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:20 Nsanja ya Olonda,5/1/1995, ptsa. 12-13
20 Azichita zimenezi kuti mtima wake usadzikweze pamaso pa abale ake,+ komanso kuti asachoke pachilamulo mwa kupatukira kudzanja lamanja kapena lamanzere.+ Azichita zimenezi kuti iyeyo ndi ana ake atalikitse masiku a ufumu wawo+ mu Isiraeli.