Deuteronomo 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Ansembe achilevi, kapena kuti fuko lonse la Levi,+ asakhale ndi gawo kapena cholowa pakati pa Isiraeli. Iwo azidya nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova. Azidya cholowa chake.+
18 “Ansembe achilevi, kapena kuti fuko lonse la Levi,+ asakhale ndi gawo kapena cholowa pakati pa Isiraeli. Iwo azidya nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova. Azidya cholowa chake.+