-
Deuteronomo 26:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ukatero uzidzanena pamaso pa Yehova Mulungu wako kuti, ‘Ndachotsa chinthu chopatulika m’nyumba mwanga ndi kuchipereka kwa Mlevi, mlendo wokhala pakati pathu, mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye.+ Ndachita zimenezi mogwirizana ndi malamulo onse amene munandipatsa. Sindinaphwanye malamulo anu kapena kuwaiwala.+
-