Salimo 119:141 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 141 Kwa ena ndine wopanda pake ndi wonyozeka.+Koma sindinaiwale malamulo anu.+ Miyambo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwana wanga, usaiwale lamulo langa,+ ndipo mtima wako usunge malamulo anga.+ Machitidwe 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pambali imeneyi, ndikuyesetsa mwakhama, kuchita mozindikira+ kuti ndisapalamule kwa Mulungu kapena kwa anthu.
16 Pambali imeneyi, ndikuyesetsa mwakhama, kuchita mozindikira+ kuti ndisapalamule kwa Mulungu kapena kwa anthu.