Yoswa 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye analowetsa m’dzikomo ana awo m’malo mwa makolowo.+ Ana amenewa Yoswa anawadula khungu, chifukwa sanadulidwe pa nthawi imene anali pa ulendo.
7 Iye analowetsa m’dzikomo ana awo m’malo mwa makolowo.+ Ana amenewa Yoswa anawadula khungu, chifukwa sanadulidwe pa nthawi imene anali pa ulendo.