Yoswa 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsiku lotsatira, iwo anayamba kudya zokolola za m’dzikomo. Pa tsikuli anayamba kudya mikate yopanda chofufumitsa+ ndiponso tirigu wokazinga.
11 Tsiku lotsatira, iwo anayamba kudya zokolola za m’dzikomo. Pa tsikuli anayamba kudya mikate yopanda chofufumitsa+ ndiponso tirigu wokazinga.