Yoswa 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova wandisunga ndi moyo+ monga mmene analonjezera.+ Tsopano padutsa zaka 45 kuchokera pamene Yehova analonjeza Mose, pa nthawi imene Aisiraeli anali m’chipululu,+ ndipo lero ndili ndi zaka 85.
10 Yehova wandisunga ndi moyo+ monga mmene analonjezera.+ Tsopano padutsa zaka 45 kuchokera pamene Yehova analonjeza Mose, pa nthawi imene Aisiraeli anali m’chipululu,+ ndipo lero ndili ndi zaka 85.