Yoswa 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Malire a kum’mawa anali Nyanja Yamchere mpaka pamene mtsinje wa Yorodano umathirira m’nyanjayi. Malire a gawoli kumpoto, anakhota pagombe pamene mtsinje wa Yorodano umathirira m’nyanjayi.+
5 Malire a kum’mawa anali Nyanja Yamchere mpaka pamene mtsinje wa Yorodano umathirira m’nyanjayi. Malire a gawoli kumpoto, anakhota pagombe pamene mtsinje wa Yorodano umathirira m’nyanjayi.+