Oweruza 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zikatero, Yehova anali kuwapatsa oweruza,+ ndipo anali kuwapulumutsa m’manja mwa ofunkha.+