Oweruza 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno usiku umenewo,+ Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Nyamuka, pita kumsasa wa Amidiyani ndi kuuthira nkhondo, chifukwa ndaupereka m’manja mwako.+
9 Ndiyeno usiku umenewo,+ Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Nyamuka, pita kumsasa wa Amidiyani ndi kuuthira nkhondo, chifukwa ndaupereka m’manja mwako.+