Oweruza 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo mnzakeyo anayankha+ kuti: “Si china ayi. Imeneyi ndi nkhondo ya Gidiyoni+ mwana wa Yowasi, mwamuna wa ku Isiraeli. Mulungu woona+ wapereka Amidiyani ndi msasa wathu wonse m’manja mwake.”+
14 Pamenepo mnzakeyo anayankha+ kuti: “Si china ayi. Imeneyi ndi nkhondo ya Gidiyoni+ mwana wa Yowasi, mwamuna wa ku Isiraeli. Mulungu woona+ wapereka Amidiyani ndi msasa wathu wonse m’manja mwake.”+