Oweruza 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo mnzakeyo anayankha kuti: “Si china ayi. Imeneyi ndi nkhondo ya Gidiyoni+ mwamuna wa ku Isiraeli, mwana wa Yowasi. Mulungu wapereka Amidiyani ndi msasa wathu wonse mʼmanja mwake.”+
14 Pamenepo mnzakeyo anayankha kuti: “Si china ayi. Imeneyi ndi nkhondo ya Gidiyoni+ mwamuna wa ku Isiraeli, mwana wa Yowasi. Mulungu wapereka Amidiyani ndi msasa wathu wonse mʼmanja mwake.”+