22 Amuna 300+ aja anapitiriza kuliza malipenga,+ ndipo Yehova anachititsa Amidiyani kuukirana okhaokha mumsasa wonsewo.+ Anthu onse a mumsasawo anathawa mpaka kukafika ku Beti-sita, ndi ku Zerera mpaka kumalire kwa mzinda wa Abele-mehola+ pafupi ndi Tabati.