27 Ndiyeno Gidiyoni anagwiritsa ntchito golideyo popanga chovala cha efodi,+ chimene anachisonyeza kwa anthu mumzinda wakwawo wa Ofira.+ Pamenepo Isiraeli yense anayamba kuchilambira ngati fano,+ moti chinakhala msampha kwa Gidiyoni ndi nyumba yake.+