6 “Ndipo apange efodi wopeta ndi golide, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota, wabwino kwambiri.+
5 Ndiyeno Mika anali ndi nyumba ya milungu,+ chotero anapanga efodi+ ndi aterafi,*+ komanso anapatsa mmodzi mwa ana ake mphamvu,*+ kuti azitumikira monga wansembe wake.+