-
Oweruza 18:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Nthawi ina, ana a Dani anatumiza amuna asanu a m’banja lawo, amuna olimba mtima ochokera pakati pawo, kuchokera kumizinda ya Zora+ ndi Esitaoli+ kuti akazonde dziko ndi kuliyendera. Ndiyeno anawauza kuti: “Pitani mukaone+ dzikolo.” Choncho anafika kudera lamapiri la Efuraimu,+ mpaka kunyumba ya Mika,+ ndipo anagona kumeneko.
-