Oweruza 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako amuna 5 amene anapita kukafufuza zokhudza mzinda wa Laisi aja,+ anauza abale awowo kuti: “Kodi mukudziwa kuti mʼnyumba izi muli efodi, aterafi,* chifaniziro chosema ndi chifaniziro chachitsulo?+ Ndiyetu dziwani zochita.”
14 Kenako amuna 5 amene anapita kukafufuza zokhudza mzinda wa Laisi aja,+ anauza abale awowo kuti: “Kodi mukudziwa kuti mʼnyumba izi muli efodi, aterafi,* chifaniziro chosema ndi chifaniziro chachitsulo?+ Ndiyetu dziwani zochita.”