Oweruza 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Amuna asanuwo analowa m’nyumba ya Mika ndi kutenga chifaniziro chosema, efodi, aterafi ndi chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula.+ Atatero wansembeyo+ anawafunsa kuti: “Mukutani kodi?”
18 Amuna asanuwo analowa m’nyumba ya Mika ndi kutenga chifaniziro chosema, efodi, aterafi ndi chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula.+ Atatero wansembeyo+ anawafunsa kuti: “Mukutani kodi?”