30 Kenako ana a Dani anadziimikira chifaniziro chosema+ chija, ndipo Yonatani+ mwana wa Gerisomu,+ mwana wa Mose, pamodzi ndi ana ake, anakhala ansembe a fuko la Dani kufikira tsiku limene anthu a m’dzikolo anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.+