Ekisodo 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Patapita nthawi Zipora anabereka mwana wamwamuna ndipo Mose anati: “Dzina lake akhale Gerisomu,*+ chifukwa ndine mlendo m’dziko lino.”+ Ekisodo 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ndipo anatenganso ana aamuna awiri+ a Zipora. Mwana wina, Mose anamutcha dzina lakuti Gerisomu,*+ ndipo anati: “Chifukwa ndine mlendo m’dziko lino.”
22 Patapita nthawi Zipora anabereka mwana wamwamuna ndipo Mose anati: “Dzina lake akhale Gerisomu,*+ chifukwa ndine mlendo m’dziko lino.”+
3 ndipo anatenganso ana aamuna awiri+ a Zipora. Mwana wina, Mose anamutcha dzina lakuti Gerisomu,*+ ndipo anati: “Chifukwa ndine mlendo m’dziko lino.”