Ekisodo 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ndipo anatenganso ana aamuna awiri+ a Zipora. Mwana wina, Mose anamutcha dzina lakuti Gerisomu,*+ ndipo anati: “Chifukwa ndine mlendo m’dziko lino.” 1 Mbiri 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ana a Mose anali Gerisomu+ ndi Eliezere.+
3 ndipo anatenganso ana aamuna awiri+ a Zipora. Mwana wina, Mose anamutcha dzina lakuti Gerisomu,*+ ndipo anati: “Chifukwa ndine mlendo m’dziko lino.”