Ekisodo 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Ndipo apange efodi wopeta ndi golide, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota, wabwino kwambiri.+ Oweruza 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiyeno Gidiyoni anagwiritsa ntchito golideyo popanga chovala cha efodi,+ chimene anachisonyeza kwa anthu mumzinda wakwawo wa Ofira.+ Pamenepo Isiraeli yense anayamba kuchilambira ngati fano,*+ moti chinakhala msampha kwa Gidiyoni ndi nyumba yake.+
6 “Ndipo apange efodi wopeta ndi golide, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota, wabwino kwambiri.+
27 Ndiyeno Gidiyoni anagwiritsa ntchito golideyo popanga chovala cha efodi,+ chimene anachisonyeza kwa anthu mumzinda wakwawo wa Ofira.+ Pamenepo Isiraeli yense anayamba kuchilambira ngati fano,*+ moti chinakhala msampha kwa Gidiyoni ndi nyumba yake.+