Genesis 31:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pa nthawiyi n’kuti Labani atapita kukameta ubweya wa nkhosa zake. Akali kumeneko, Rakele anaba aterafi*+ a bambo ake. Oweruza 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno amuna asanu amene anapita kukazonda+ dziko la Laisi+ aja, anauza abale awo kuti: “Kodi mukudziwa kuti m’nyumba izi muli efodi, aterafi,+ chifaniziro chosema+ ndi chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula?+ Ndiyetu dziwani chochita.”+ Hoseya 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ziyenera kukhala choncho chifukwa chakuti kwa masiku ambiri, ana a Isiraeli adzakhala opanda mfumu,+ kalonga, nsembe,+ chipilala chopatulika, efodi,+ ndi aterafi.*+
19 Pa nthawiyi n’kuti Labani atapita kukameta ubweya wa nkhosa zake. Akali kumeneko, Rakele anaba aterafi*+ a bambo ake.
14 Ndiyeno amuna asanu amene anapita kukazonda+ dziko la Laisi+ aja, anauza abale awo kuti: “Kodi mukudziwa kuti m’nyumba izi muli efodi, aterafi,+ chifaniziro chosema+ ndi chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula?+ Ndiyetu dziwani chochita.”+
4 Ziyenera kukhala choncho chifukwa chakuti kwa masiku ambiri, ana a Isiraeli adzakhala opanda mfumu,+ kalonga, nsembe,+ chipilala chopatulika, efodi,+ ndi aterafi.*+