Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 31:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pamenepo Rakele ndi Leya anamuyankha kuti: “Kodi ifeyo tatsala ndi cholowa chilichonse m’nyumba ya bambo athu ngati?+

  • Genesis 31:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Ngati wachoka chifukwa cholakalaka kwambiri kunyumba kwa bambo ako, nanga n’chifukwa chiyani waba milungu yanga?”+

  • Genesis 35:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno Yakobo anauza anthu a m’banja lake ndi onse amene anali naye kuti: “Chotsani milungu yachilendo imene ili pakati panu.+ Dziyeretseni ndipo sinthani zovala zanu.+

  • Yoswa 24:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tsopano Yoswa anauza anthu onse kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Kalekale, makolo anu,+ kuphatikizapo Tera, bambo ake a Abulahamu ndi Nahori,+ ankakhala kutsidya lina la Mtsinje,*+ ndipo ankatumikira milungu ina.

  • Ezekieli 21:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Mfumu ya Babulo yaima chilili pamene panakumana misewu iwiri kuti iwombeze maula.+ Mfumuyo yagwedeza mivi, yafunsira kwa aterafi*+ ndi kuyang’ana pachiwindi cha nyama.

  • Zekariya 10:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Aterafi*+ amalankhula zoipa. Ochita zamaula amaona masomphenya onama+ ndipo amafotokoza maloto opanda pake. Iwo saphula kanthu polimbikitsa anthu.+ N’chifukwa chake adzasochere ngati nkhosa.+ Iwo adzavutika chifukwa adzakhala opanda m’busa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena