Genesis 31:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pa nthawiyi n’kuti Labani atapita kukameta ubweya wa nkhosa zake. Akali kumeneko, Rakele anaba aterafi*+ a bambo ake. Deuteronomo 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Usakhale ndi milungu ina iliyonse motsutsana ndi ine.+ Yoswa 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso musayanjane ndi mitundu+ imene yatsala pakati panu. Musamatchule mayina a milungu yawo+ kapena kulumbirira pa milunguyo,+ ndipo musamaitumikire kapena kuigwadira.+ 1 Akorinto 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiye chifukwa chake, okondedwa anga, thawani+ kupembedza mafano.+
19 Pa nthawiyi n’kuti Labani atapita kukameta ubweya wa nkhosa zake. Akali kumeneko, Rakele anaba aterafi*+ a bambo ake.
7 Ndiponso musayanjane ndi mitundu+ imene yatsala pakati panu. Musamatchule mayina a milungu yawo+ kapena kulumbirira pa milunguyo,+ ndipo musamaitumikire kapena kuigwadira.+