28 Pamenepo Gaala mwana wa Ebedi anati: “Abimeleki ndani,+ ndipo Sekemu ndani kuti tim’tumikire? Kodi iye si mwana wa Yerubaala,+ ndipo mtumiki wake si Zebuli?+ Ena nonsenu tumikirani ana a Hamori,+ bambo a Sekemu, koma ifeyo tim’tumikire chifukwa chiyani?