Oweruza 9:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Pamenepo Abimeleki anapita kunsanjayo ndi kuyamba kumenyana ndi anthu amene anali mmenemo. Ndiyeno anayandikira khomo la nsanjayo kuti aitenthe ndi moto.+
52 Pamenepo Abimeleki anapita kunsanjayo ndi kuyamba kumenyana ndi anthu amene anali mmenemo. Ndiyeno anayandikira khomo la nsanjayo kuti aitenthe ndi moto.+