Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 9:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Zitatero Abimeleki anakwera phiri la Zalimoni+ pamodzi ndi anthu onse amene anali naye. Tsopano Abimeleki anatenga nkhwangwa m’manja mwake, n’kudula nthambi ya mtengo, ndipo nthambiyo anainyamula n’kuiika paphewa lake. Pamenepo anauza anthu amene anali naye kuti: “Zimene mwaona ine ndikuchita, muchitenso zomwezo mofulumira!”+

  • Oweruza 9:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Chotero anthu onsewo, aliyense wa iwo anadula nthambi yake ndi kutsatira Abimeleki. Kenako anatsamiritsa nthambizo pachipinda chotetezekacho n’kuchiyatsa moto, moti nawonso anthu onse okhala munsanja ya Sekemu, amuna ndi akazi pafupifupi 1,000, anafa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena