Oweruza 9:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Chotero Mulungu anachititsa zoipa zimene Abimeleki anachitira bambo ake mwa kupha abale ake 70, kum’bwerera pamutu pake.+
56 Chotero Mulungu anachititsa zoipa zimene Abimeleki anachitira bambo ake mwa kupha abale ake 70, kum’bwerera pamutu pake.+