Oweruza 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nditaona kuti inu simukubwera kudzandipulumutsa, ndinalolera kufa,* moti ndinapita kukamenyana ndi ana a Amoni,+ ndipo Yehova anawapereka m’manja mwanga.+ Tsopano n’chifukwa chiyani lero mwabwera kudzandiukira kuti mumenyane nane?” Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:3 Nsanja ya Olonda,5/15/2007, tsa. 10
3 Nditaona kuti inu simukubwera kudzandipulumutsa, ndinalolera kufa,* moti ndinapita kukamenyana ndi ana a Amoni,+ ndipo Yehova anawapereka m’manja mwanga.+ Tsopano n’chifukwa chiyani lero mwabwera kudzandiukira kuti mumenyane nane?”