1 Samueli 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Oponya mivi ndi uta mwaluso agwidwa ndi mantha,+Koma olefuka apeza mphamvu zochuluka.+