1 Samueli 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Samueli anauza Sauli kuti: “Yehova anatuma ine kudzakudzoza+ kukhala mfumu ya anthu ake Aisiraeli, choncho imva zimene Yehova wanena.+
15 Ndiyeno Samueli anauza Sauli kuti: “Yehova anatuma ine kudzakudzoza+ kukhala mfumu ya anthu ake Aisiraeli, choncho imva zimene Yehova wanena.+