1 Samueli 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Patapita nthawi, uthenga unafika kwa Sauli wonena kuti Davide anathawira ku Gati. Atamva zimenezo sanapitenso kukam’sakasaka.+
4 Patapita nthawi, uthenga unafika kwa Sauli wonena kuti Davide anathawira ku Gati. Atamva zimenezo sanapitenso kukam’sakasaka.+