1 Samueli 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho udzuke m’mawa kwambiri pamodzi ndi atumiki a mbuye wako amene anabwera nawe pamodzi. Mukangoona kuti kwayera mudzuke ndi kunyamuka.”+
10 Choncho udzuke m’mawa kwambiri pamodzi ndi atumiki a mbuye wako amene anabwera nawe pamodzi. Mukangoona kuti kwayera mudzuke ndi kunyamuka.”+