2 Samueli 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mwana+ wa Sauli atamva kuti Abineri wafa ku Heburoni,+ manja ake analefuka+ ndipo Aisiraeli onse anasokonezeka.
4 Mwana+ wa Sauli atamva kuti Abineri wafa ku Heburoni,+ manja ake analefuka+ ndipo Aisiraeli onse anasokonezeka.