2 Samueli 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndimupeza ali wotopa ndi wofooka manja ake onse,+ ndipo adzanjenjemera ndithu chifukwa cha ine. Pamenepo anthu onse amene ali naye adzathawa, ndipo ine ndidzapha mfumu ili yokha.+ Ezara 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kuyambira pamenepo, anthu a m’dzikolo anakhala akufooketsa+ manja a anthu a ku Yuda ndi kuwagwetsa ulesi pa ntchito yomanga.+ Yesaya 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 N’chifukwa chake anthu onse adzataya mtima, ndipo mitima ya anthu onse idzasungunuka.+
2 Ndimupeza ali wotopa ndi wofooka manja ake onse,+ ndipo adzanjenjemera ndithu chifukwa cha ine. Pamenepo anthu onse amene ali naye adzathawa, ndipo ine ndidzapha mfumu ili yokha.+
4 Kuyambira pamenepo, anthu a m’dzikolo anakhala akufooketsa+ manja a anthu a ku Yuda ndi kuwagwetsa ulesi pa ntchito yomanga.+