1 Mafumu 22:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Mfumu ya Siriya inali italamula akuluakulu ake 32+ oyang’anira asilikali okwera magaleta, kuti: “Musakamenyane ndi wina aliyense, wamng’ono kapena wamkulu, koma mfumu ya Isiraeli yokha basi.”+ Salimo 37:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Woipa akukonzera chiwembu munthu wolungama,+Ndipo akumukukutira mano.+ Salimo 41:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma munthu amene ndinali kukhala naye mwamtendere, amene ndinali kumukhulupirira,+Munthu amene anali kudya chakudya changa,+ wakweza chidendene chake kundiukira.+ Salimo 55:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti amene ananditonza si mdani.+Akanakhala mdani ndikanapirira.Amene anadzikweza pamaso panga si munthu wodana nane kwambiri.+Akanakhala munthu wodana nane kwambiri ndikanabisala.+
31 Mfumu ya Siriya inali italamula akuluakulu ake 32+ oyang’anira asilikali okwera magaleta, kuti: “Musakamenyane ndi wina aliyense, wamng’ono kapena wamkulu, koma mfumu ya Isiraeli yokha basi.”+
9 Koma munthu amene ndinali kukhala naye mwamtendere, amene ndinali kumukhulupirira,+Munthu amene anali kudya chakudya changa,+ wakweza chidendene chake kundiukira.+
12 Pakuti amene ananditonza si mdani.+Akanakhala mdani ndikanapirira.Amene anadzikweza pamaso panga si munthu wodana nane kwambiri.+Akanakhala munthu wodana nane kwambiri ndikanabisala.+