2 Mbiri 18:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mfumu ya Siriya inali italamula akuluakulu ake oyang’anira asilikali okwera magaleta, kuti: “Musakamenyane ndi wina aliyense, wamng’ono kapena wamkulu, koma mfumu ya Isiraeli yokha basi.”+
30 Mfumu ya Siriya inali italamula akuluakulu ake oyang’anira asilikali okwera magaleta, kuti: “Musakamenyane ndi wina aliyense, wamng’ono kapena wamkulu, koma mfumu ya Isiraeli yokha basi.”+