1 Mafumu 22:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Mfumu ya Siriya inali italamula akuluakulu ake 32+ oyang’anira asilikali okwera magaleta, kuti: “Musakamenyane ndi wina aliyense, wamng’ono kapena wamkulu, koma mfumu ya Isiraeli yokha basi.”+ Miyambo 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iweyo udzatha kumenya nkhondo yako potsatira malangizo anzeru,+ ndipo pakakhala aphungu ochuluka anthu amapulumuka.+
31 Mfumu ya Siriya inali italamula akuluakulu ake 32+ oyang’anira asilikali okwera magaleta, kuti: “Musakamenyane ndi wina aliyense, wamng’ono kapena wamkulu, koma mfumu ya Isiraeli yokha basi.”+
6 Iweyo udzatha kumenya nkhondo yako potsatira malangizo anzeru,+ ndipo pakakhala aphungu ochuluka anthu amapulumuka.+