Ezara 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero iwo anamanga guwa lansembe lolimba pamalo ake+ akale, chifukwa anali kuopa anthu a mitundu ina.+ Atatero anayamba kuperekerapo nsembe zopsereza kwa Yehova, zam’mawa ndi zamadzulo.+ Nehemiya 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Onsewo anali kungofuna kutichititsa mantha, ndipo anali kunena kuti: “Manja awo+ adzalefuka ndipo adzasiya kugwira ntchitoyi, mwakuti siitha.” Inu Mulungu wanga, limbitsani manja anga.+
3 Chotero iwo anamanga guwa lansembe lolimba pamalo ake+ akale, chifukwa anali kuopa anthu a mitundu ina.+ Atatero anayamba kuperekerapo nsembe zopsereza kwa Yehova, zam’mawa ndi zamadzulo.+
9 Onsewo anali kungofuna kutichititsa mantha, ndipo anali kunena kuti: “Manja awo+ adzalefuka ndipo adzasiya kugwira ntchitoyi, mwakuti siitha.” Inu Mulungu wanga, limbitsani manja anga.+