1 Mbiri 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno mngelo wa Yehova anauza Gadi+ kuti auze Davide kuti Davideyo apite kumalo opunthira mbewu a Orinani Myebusi, n’kukamanga guwa lansembe la Yehova.+
18 Ndiyeno mngelo wa Yehova anauza Gadi+ kuti auze Davide kuti Davideyo apite kumalo opunthira mbewu a Orinani Myebusi, n’kukamanga guwa lansembe la Yehova.+