Ezara 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kuyambira pamenepo, anthu a m’dzikolo anakhala akufooketsa+ manja a anthu a ku Yuda ndi kuwagwetsa ulesi pa ntchito yomanga.+ Salimo 56:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine ndidzadalira inu, tsiku lililonse limene ndingachite mantha.+ Miyambo 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kuopa anthu n’kumene kumatchera msampha,+ koma wokhulupirira Yehova adzatetezedwa.+
4 Kuyambira pamenepo, anthu a m’dzikolo anakhala akufooketsa+ manja a anthu a ku Yuda ndi kuwagwetsa ulesi pa ntchito yomanga.+