Numeri 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mwana wa nkhosa mmodzi wamphongo muzim’pereka nsembe m’mawa. Ndipo mwana wa nkhosa wamphongo winayo, muzim’pereka nsembe madzulo kuli kachisisira.*+ Numeri 28:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Muzipereka nsembe zimenezi, kuwonjezera pa nsembe yopsereza+ ya m’mawa ya tsiku ndi tsiku.+
4 Mwana wa nkhosa mmodzi wamphongo muzim’pereka nsembe m’mawa. Ndipo mwana wa nkhosa wamphongo winayo, muzim’pereka nsembe madzulo kuli kachisisira.*+