Ekisodo 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nkhosayo muisunge kufikira tsiku la 14 la mwezi uno.+ Kenako banja lililonse la Isiraeli lidzaphe nkhosa yawo madzulo kuli kachisisira.*+ Ekisodo 29:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Uzipereka mwana wa nkhosa mmodzi m’mawa,+ ndipo mwana wa nkhosa winayo madzulo kuli kachisisira.*+ Deuteronomo 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma uzipereka nsembe ya pasikayo pamalo amene Yehova Mulungu wako adzasankhe kuikapo dzina lake.+ Uzipereka nsembeyo madzulo, dzuwa likangolowa,+ pa nthawi yofanana ndi imene unatuluka mu Iguputo.
6 Nkhosayo muisunge kufikira tsiku la 14 la mwezi uno.+ Kenako banja lililonse la Isiraeli lidzaphe nkhosa yawo madzulo kuli kachisisira.*+
39 Uzipereka mwana wa nkhosa mmodzi m’mawa,+ ndipo mwana wa nkhosa winayo madzulo kuli kachisisira.*+
6 Koma uzipereka nsembe ya pasikayo pamalo amene Yehova Mulungu wako adzasankhe kuikapo dzina lake.+ Uzipereka nsembeyo madzulo, dzuwa likangolowa,+ pa nthawi yofanana ndi imene unatuluka mu Iguputo.