2 Samueli 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Davide atamva zimenezi anatumiza Yowabu ndi gulu lonse lankhondo pamodzi ndi amuna amphamvu.+